2 Mbiri 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ monga anachitira Manase bambo ake.+ Amoni anali kupereka nsembe+ kwa zifaniziro zonse zogoba+ zimene bambo ake+ anapanga, ndipo anapitiriza kuzitumikira.+
22 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ monga anachitira Manase bambo ake.+ Amoni anali kupereka nsembe+ kwa zifaniziro zonse zogoba+ zimene bambo ake+ anapanga, ndipo anapitiriza kuzitumikira.+