Salimo 41:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+Kuyambira kalekale mpaka kalekale.+Ame! Ame!*+ Salimo 145:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ntchito zanu zonse zidzakutamandani, inu Yehova,+Ndipo okhulupirika anu adzakutamandani.+ Yakobo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti lilime timatamanda nalo Yehova,+ amenenso ndi Atate,+ komanso ndi lilime lomwelo timatemberera+ anthu amene analengedwa “m’chifaniziro cha Mulungu.”+
9 Pakuti lilime timatamanda nalo Yehova,+ amenenso ndi Atate,+ komanso ndi lilime lomwelo timatemberera+ anthu amene analengedwa “m’chifaniziro cha Mulungu.”+