Salimo 75:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mulungu ndiye woweruza.+Amatsitsa wina ndi kukweza wina.+ Danieli 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inuyo mfumu, mfumu ya mafumu, inu amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu, ndi ulemerero, Danieli 4:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+ Danieli 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mfumu, Mulungu Wam’mwambamwamba+ anapatsa bambo anu+ Nebukadinezara ufumu, ukulu, ulemu ndi ulemerero.+
37 Inuyo mfumu, mfumu ya mafumu, inu amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu, ndi ulemerero,
35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+
18 Inu mfumu, Mulungu Wam’mwambamwamba+ anapatsa bambo anu+ Nebukadinezara ufumu, ukulu, ulemu ndi ulemerero.+