9 Atatero anayamba kusonkhanitsa pamodzi Ayuda ndi Abenjamini+ onse, ndi alendo ambirimbiri+ amene anali pakati pawo ochokera ku fuko la Efuraimu, Manase ndi Simiyoni. Alendowa anathawa ku Isiraeli n’kubwera kwa iye ataona kuti Yehova Mulungu wake ali naye.+