-
1 Mafumu 14:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Rehobowamu+ mwana wa Solomo anali atakhala mfumu ku Yuda. Rehobowamu anali ndi zaka 41 pamene anayamba kulamulira, ndipo kwa zaka 17 analamulira ku Yerusalemu, mzinda+ umene Yehova anasankha pakati pa mafuko onse+ a Isiraeli kuti aike dzina lake kumeneko.+ Mayi ake dzina lawo linali Naama Muamoni.+
-