Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 ‘Kuchokera tsiku limene ndinatulutsa anthu anga Aisiraeli m’dziko la Iguputo, sindinasankhe+ mzinda m’mafuko onse a Isiraeli woti iwo amangeko nyumba+ ya dzina langa+ kuti likhale kumeneko. Koma ndidzasankha Davide kuti alamulire anthu anga Aisiraeli.’+

  • 1 Mafumu 11:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Mwana wake ndidzam’patsa fuko limodzi kuti Davide mtumiki wanga apitirize kukhala ndi nyale pamaso panga mu Yerusalemu,+ mzinda umene ndausankha kuti ndiikepo dzina langa.+

  • 2 Mbiri 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mfumu Rehobowamu inapitiriza kulimbitsa ufumu wake ndi kulamulira ku Yerusalemu. Rehobowamu+ anali ndi zaka 41 pamene anayamba kulamulira, ndipo kwa zaka 17 analamulira ku Yerusalemu, mzinda+ umene Yehova anasankha pakati pa mafuko onse a Isiraeli kuti aike dzina lake kumeneko.+ Mayi ake dzina lawo linali Naama+ Muamoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena