Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Muamoni kapena Mmowabu asalowe mumpingo wa Yehova.+ Ana awo asalowe mumpingo wa Yehova kufikira m’badwo wa 10, ngakhalenso mpaka kalekale.

  • 1 Mafumu 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mfumu Solomo inakonda akazi ambiri achilendo+ kuphatikiza pa mwana wamkazi wa Farao.+ Inakonda akazi achimowabu,+ achiamoni,+ achiedomu,+ achisidoni,+ ndi achihiti.+

  • Nehemiya 13:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kodi si akazi amenewa amene anachimwitsa Solomo mfumu ya Isiraeli?+ Mwa mitundu yonse panalibe mfumu yofanana naye.+ Iye anakondedwa ndi Mulungu wake,+ mwakuti Mulungu anamuika kukhala mfumu ya Isiraeli yense. Koma akazi achilendo anamuchimwitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena