1 Mbiri 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Funafunani Yehova ndiponso mphamvu zake,+Funafunani nkhope yake+ nthawi zonse. Salimo 105:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyadirani dzina lake loyera.+Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale.+