2 Mbiri 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova anachititsa kuti ufumuwo ukhazikike m’manja mwake+ ndipo Ayuda onse anapitiriza kupereka+ mphatso kwa Yehosafati. Chotero iye anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero wochuluka.+
5 Yehova anachititsa kuti ufumuwo ukhazikike m’manja mwake+ ndipo Ayuda onse anapitiriza kupereka+ mphatso kwa Yehosafati. Chotero iye anakhala ndi chuma chambiri ndi ulemerero wochuluka.+