1 Mbiri 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Onse amene anasankhidwa kuti akhale alonda a pamakomo analipo 212. Iwo anakhala m’midzi yawo+ mogwirizana ndi mndandanda wa mayina wotsatira makolo awo.+ Davide+ ndi Samueli wamasomphenya+ anaika amenewa pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo.+ 1 Mbiri 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pa alonda a pazipatawo panali amuna anayi amphamvu amene anali pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo. Amunawo anali Alevi, ndipo anali kuyang’anira zipinda zodyera+ ndi chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona.
22 Onse amene anasankhidwa kuti akhale alonda a pamakomo analipo 212. Iwo anakhala m’midzi yawo+ mogwirizana ndi mndandanda wa mayina wotsatira makolo awo.+ Davide+ ndi Samueli wamasomphenya+ anaika amenewa pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo.+
26 Pa alonda a pazipatawo panali amuna anayi amphamvu amene anali pa udindo wawo chifukwa cha kukhulupirika kwawo. Amunawo anali Alevi, ndipo anali kuyang’anira zipinda zodyera+ ndi chuma+ cha m’nyumba ya Mulungu woona.