Ezara 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Inu mfumu dziwani kuti ife tinapita kuchigawo+ cha Yuda kunyumba ya Mulungu wamkulu.+ Kumeneko takapeza kuti nyumbayo akuimanga ndi miyala yochita kuigubuduzira pamalo ake ndiponso akuika matabwa m’makoma ake. Iwo akugwira ntchitoyo mwakhama ndipo ikupita patsogolo. Danieli 2:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mfumuyo inauza Danieli kuti: “Ndithudi Mulungu wa anthu inu ndi Mulungu wa milungu yonse,+ Ambuye wa mafumu onse+ ndiponso Woulula zinsinsi, chifukwa iwe wakwanitsa kuulula chinsinsi chimenechi.”+
8 Inu mfumu dziwani kuti ife tinapita kuchigawo+ cha Yuda kunyumba ya Mulungu wamkulu.+ Kumeneko takapeza kuti nyumbayo akuimanga ndi miyala yochita kuigubuduzira pamalo ake ndiponso akuika matabwa m’makoma ake. Iwo akugwira ntchitoyo mwakhama ndipo ikupita patsogolo.
47 Mfumuyo inauza Danieli kuti: “Ndithudi Mulungu wa anthu inu ndi Mulungu wa milungu yonse,+ Ambuye wa mafumu onse+ ndiponso Woulula zinsinsi, chifukwa iwe wakwanitsa kuulula chinsinsi chimenechi.”+