Oweruza 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mngelo wa Yehova+ anati: ‘Tembererani+ Merozi,Tembererani anthu ake mosaleka,Chifukwa sanathandize Yehova,Sanabwere ndi anthu amphamvu kudzathandiza Yehova.’ Luka 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Amene sali kumbali yanga akutsutsana ndi ine, ndipo amene sasonkhanitsa anthu pamodzi ndi ine amawabalalitsa.+ 1 Timoteyo 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+
23 Mngelo wa Yehova+ anati: ‘Tembererani+ Merozi,Tembererani anthu ake mosaleka,Chifukwa sanathandize Yehova,Sanabwere ndi anthu amphamvu kudzathandiza Yehova.’
23 Amene sali kumbali yanga akutsutsana ndi ine, ndipo amene sasonkhanitsa anthu pamodzi ndi ine amawabalalitsa.+
17 Lamula achuma+ a m’nthawi* ino kuti asakhale odzikweza,+ ndiponso kuti asamadalire chuma chosadalirika,+ koma adalire Mulungu, amene amatipatsa mowolowa manja zinthu zonse kuti tisangalale.+