Miyambo 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndi bwino kusankha dzina labwino kusiyana ndi chuma chochuluka.+ Kulemekezedwa kuli bwino kuposa siliva ndi golide.+ Mlaliki 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mbiri yabwino imaposa mafuta onunkhira,+ ndipo tsiku lomwalira limaposa tsiku lobadwa.+
22 Ndi bwino kusankha dzina labwino kusiyana ndi chuma chochuluka.+ Kulemekezedwa kuli bwino kuposa siliva ndi golide.+