4 Pamenepo ndinayamba kupemphera kwa Yehova Mulungu wanga ndi kuvomereza machimo athu kuti:+
“Inu Yehova Mulungu woona, Mulungu wamkulu+ ndi wochititsa mantha. Anthu amene amakukondani ndi kusunga malamulo anu+ mumawasungira pangano+ ndi kuwasonyeza kukoma mtima kosatha.+