Ekisodo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pokumbukira kuti muyenera kusunga tsiku la sabata ndi kuliona kukhala lopatulika,+ Ekisodo 31:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Muzisunga sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Amene walinyoza ayenera kuphedwa ndithu.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+
14 Muzisunga sabata chifukwa ndi lopatulika kwa inu.+ Amene walinyoza ayenera kuphedwa ndithu.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.+