Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+ Salimo 55:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+Ndipo iye adzakuchirikiza.+Sadzalola kuti wolungama agwedezeke.+ Salimo 62:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.] Salimo 115:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Isiraeli, khulupirira Yehova.+Iye ndiye thandizo lako ndi chishango chako.+ Miyambo 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuopa anthu n’kumene kumatchera msampha,+ koma wokhulupirira Yehova adzatetezedwa.+ Aroma 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anaika miyoyo+ yawo pachiswe chifukwa cha moyo wanga, ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira,+ komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina.
8 Mukhulupirireni nthawi zonse, anthu inu.+Mukhuthulireni za mumtima mwanu.+Mulungu ndiye pothawirapo pathu.+ [Seʹlah.]
4 Iwo anaika miyoyo+ yawo pachiswe chifukwa cha moyo wanga, ndipo si ine ndekha amene ndikuwayamikira,+ komanso mipingo yonse ya anthu a mitundu ina.