-
Esitere 2:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno nthawi itakwana yoti Esitere akaonekere kwa mfumu, sanapemphe kalikonse+ kupatulapo zimene Hegai+ anatchula. Iye anali munthu wofulidwa wa mfumu woyang’anira akazi, amenenso anali mkulu woyang’anira nyumba ya akazi. Esitere anali mwana wa Abihaili, m’bale wa bambo ake a Moredekai, amene Moredekai anamutenga ngati mwana wake+ (pa nthawi imeneyi Esitere anali kukondedwa ndi aliyense womuona).+
-