2 Samueli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+ Salimo 55:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye adzandiwombola ndi kundikhazika pa mtendere, kundichotsa pankhondo,+Pakuti khamu la anthu landiukira.+
9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi m’bale wake Bana, ana a Rimoni Mbeeroti kuti: “Pali Yehova Mulungu wamoyo,+ amene anawombola+ moyo wanga+ m’masautso anga onse,+
18 Iye adzandiwombola ndi kundikhazika pa mtendere, kundichotsa pankhondo,+Pakuti khamu la anthu landiukira.+