Deuteronomo 32:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+ Yeremiya 17:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwa kufuna kwanu munataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Inenso ndidzakuchititsani kutumikira adani anu m’dziko limene simunalidziwe.+ Anthu inu, ndakuyatsani ndi mkwiyo wanga+ ndipo moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”
22 Pakuti pa kukwiya kwanga moto wayaka,+Ndipo udzayaka mpaka kukafika ku Manda,* malo a pansi penipeni.+Udzanyeketsa dziko lapansi ndi zipatso zake,+Ndi kuyatsa maziko a mapiri.+
4 Mwa kufuna kwanu munataya cholowa chimene ndinakupatsani.+ Inenso ndidzakuchititsani kutumikira adani anu m’dziko limene simunalidziwe.+ Anthu inu, ndakuyatsani ndi mkwiyo wanga+ ndipo moto wake udzayakabe mpaka kalekale.”