Yobu 26:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi mphamvu zake wavundula nyanja,+Ndipo ndi kuzindikira kwake wathyolathyola+ wachiwawa.*+ Yesaya 51:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,+ iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati m’mibadwo yakalekale.+ Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,+ amene unabaya* chilombo cha m’nyanja?+
9 Dzuka! Dzuka! Vala mphamvu,+ iwe dzanja la Yehova!+ Dzuka ngati masiku akale, ngati m’mibadwo yakalekale.+ Kodi si iwe amene unaphwanyaphwanya Rahabi,+ amene unabaya* chilombo cha m’nyanja?+