1 Mafumu 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho uyu anayamba kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+ Miyambo 8:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Tsiku ndi tsiku, iye anali kusangalala kwambiri ndi ine.+ Ineyo ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+ Amosi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+
20 Kenako Yehova anati, ‘Ndani akapusitse Ahabu, kuti apite ku Ramoti-giliyadi n’kukafa?’ Choncho uyu anayamba kunena zakutizakuti, uyunso n’kumanena zakutizakuti.+
30 ine ndinali pambali pake monga mmisiri waluso.+ Tsiku ndi tsiku, iye anali kusangalala kwambiri ndi ine.+ Ineyo ndinkakhala wosangalala pamaso pake nthawi zonse.+
7 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, sangachite kalikonse asanaulule chinsinsi chake kwa atumiki ake, aneneri.+