Yesaya 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsoka kwa amene akunena kuti chabwino n’choipa ndipo choipa n’chabwino,+ amene akuika mdima m’malo mwa kuwala ndi kuwala m’malo mwa mdima, amene akuika zowawa m’malo mwa zotsekemera,* ndi zotsekemera m’malo mwa zowawa.+ Yohane 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.
20 Tsoka kwa amene akunena kuti chabwino n’choipa ndipo choipa n’chabwino,+ amene akuika mdima m’malo mwa kuwala ndi kuwala m’malo mwa mdima, amene akuika zowawa m’malo mwa zotsekemera,* ndi zotsekemera m’malo mwa zowawa.+
19 Tsopano maziko operekera chiweruzo ndi awa, kuwala+ kwafika m’dziko+ koma anthu akonda mdima m’malo mwa kuwala,+ pakuti ntchito zawo n’zoipa.