Salimo 55:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+ Miyambo 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+ Yakobo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+
21 Mawu a pakamwa pake ndi osalala ngati mafuta a mkaka,+Koma mtima wake umakonda ndewu.+Mawu ake ndi osalala ngati mafuta,+Koma ali ngati lupanga lakuthwa.+
18 Pali munthu amene amalankhula mosaganizira ndi mawu olasa ngati lupanga,+ koma lilime la anthu anzeru limachiritsa.+
8 Koma lilime, palibe munthu ndi mmodzi yemwe angathe kuliweta. Ndilo kanthu kamodzi kosalamulirika ndi kovulaza, kodzaza ndi poizoni wakupha.+