Yesaya 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+ Amosi 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Akakumba Manda* kuti abisale mmenemo ndidzawatulutsa ndi dzanja langa,+ ndipo akakwera kumwamba ndidzawatsitsira pansi.+ Obadiya 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova.
13 Iweyo wanena mumtima mwako kuti, ‘Ndikwera kumwamba.+ Ndikweza mpando wanga wachifumu+ pamwamba pa nyenyezi+ za Mulungu. Ndikhala paphiri lokumanapo+ kumapeto kwenikweni kwa madera a kumpoto.+
2 Akakumba Manda* kuti abisale mmenemo ndidzawatulutsa ndi dzanja langa,+ ndipo akakwera kumwamba ndidzawatsitsira pansi.+
4 Ngakhale malo ako atakhala pamwamba ngati a chiwombankhanga, kapena ngakhale utamanga chisa chako pakati pa nyenyezi, ine ndidzakugwetsa kuchokera pamenepo,”+ watero Yehova.