Yobu 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yobu anatenga phale loti azidzikanda nalo ndipo anali kukhala paphulusa.+ Yobu 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anakhala+ naye limodzi pansi masiku 7 usana ndi usiku, ndipo palibe amene anali kumulankhula chilichonse popeza iwo anaona kuti ululu+ wake unali waukulu kwambiri. Yobu 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndikagona ndimanena kuti, ‘Kodi ndidzuka nthawi yanji?’+Kukada ndimangokhalira kutembenukatembenuka mpaka m’mawa kuli mbuu.
13 Kenako anakhala+ naye limodzi pansi masiku 7 usana ndi usiku, ndipo palibe amene anali kumulankhula chilichonse popeza iwo anaona kuti ululu+ wake unali waukulu kwambiri.
4 Ndikagona ndimanena kuti, ‘Kodi ndidzuka nthawi yanji?’+Kukada ndimangokhalira kutembenukatembenuka mpaka m’mawa kuli mbuu.