Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu,+ poti palibe wina wokhala ngati iyeyo padziko lapansi? Iyetu ndi munthu wopanda cholakwa ndi wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+ Komabe iye akadali ndi mtima wosagawanika+ ngakhale kuti iweyo ukundiumiriza+ kuti ndimuwononge popanda chifukwa.”+

  • Ezekieli 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 ngakhale Nowa,+ Danieli+ ndi Yobu+ akanakhala m’dzikolo,+ pali ine Mulungu wamoyo, sakanapulumutsamo mwana wawo wamwamuna kapena wamkazi. Iwo okhawo akanapulumutsa miyoyo yawo chifukwa chokhala olungama,’ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”+

  • Yakobo 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Monga mmene mukudziwira, anthu amene anapirira timawatcha odala.+ Munamva za kupirira kwa Yobu+ ndipo mwaona zimene Yehova anamupatsa,+ mwaona kuti Yehova ndi wachikondi chachikulu ndi wachifundo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena