Mika 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kodi nditenge chiyani popita kukakumana+ ndi Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba?+ Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu+ ndi ana a ng’ombe achaka chimodzi?
6 Kodi nditenge chiyani popita kukakumana+ ndi Yehova? Ndikagwade ndi chiyani kwa Mulungu wakumwamba?+ Kodi ndipite nditatenga nsembe zopsereza zathunthu+ ndi ana a ng’ombe achaka chimodzi?