Yeremiya 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Musamakhulupirire mawu achinyengo+ ndi kunena kuti, ‘Nyumba izi ndizo kachisi wa Yehova, inde ndi kachisi wa Yehova, ndithudi ndi kachisi wa Yehova!’ Mateyu 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ine ndidzawauza momveka bwino kuti: Sindikukudziwani ngakhale pang’ono!+ Chokani pamaso panga, anthu osamvera malamulo inu.+ Aroma 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 kodi iwe wophunzitsa enawe, sudziphunzitsa wekha?+ Iwe amene umalalikira kuti “Usabe,”+ umabanso kodi?+
4 Musamakhulupirire mawu achinyengo+ ndi kunena kuti, ‘Nyumba izi ndizo kachisi wa Yehova, inde ndi kachisi wa Yehova, ndithudi ndi kachisi wa Yehova!’
23 Koma ine ndidzawauza momveka bwino kuti: Sindikukudziwani ngakhale pang’ono!+ Chokani pamaso panga, anthu osamvera malamulo inu.+
21 kodi iwe wophunzitsa enawe, sudziphunzitsa wekha?+ Iwe amene umalalikira kuti “Usabe,”+ umabanso kodi?+