Genesis 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chotero, Mulungu poyang’ana dziko lapansi anaona kuti laipa,+ chifukwa njira za anthu onse zinali zitaipa.+ Salimo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu. Salimo 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Onse apatuka,+ ndipo onsewo ndi achinyengo.+Palibe aliyense amene akuchita zabwino,+Palibiretu ndi mmodzi yemwe.+ Mlaliki 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Palibe munthu wolungama padziko lapansi amene amachita zabwino zokhazokha osachimwa.+ Aroma 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu onse apanduka, onse pamodzi akhala opanda pake. Palibe amene akusonyeza kukoma mtima, palibiretu ndi mmodzi yemwe.”+
12 Chotero, Mulungu poyang’ana dziko lapansi anaona kuti laipa,+ chifukwa njira za anthu onse zinali zitaipa.+
12 Ndipulumutseni,+ inu Yehova, pakuti anthu okhulupirika atha.+Anthu okhulupirika atheratu pakati pa ana a anthu.
3 Onse apatuka,+ ndipo onsewo ndi achinyengo.+Palibe aliyense amene akuchita zabwino,+Palibiretu ndi mmodzi yemwe.+
12 Anthu onse apanduka, onse pamodzi akhala opanda pake. Palibe amene akusonyeza kukoma mtima, palibiretu ndi mmodzi yemwe.”+