Miyambo 10:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Woipa amatha ngati momwe zimakhalira pakawomba mphepo yamkuntho,+ koma wolungama ndiye maziko mpaka kalekale.*+ Yeremiya 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Taonani! Mphepo yamkuntho yochokera kwa Yehova idzawomba. Mkwiyo wake udzawomba ngati kamvulumvulu wamphamvu.+ Udzawomba pamitu ya anthu oipawo.+
25 Woipa amatha ngati momwe zimakhalira pakawomba mphepo yamkuntho,+ koma wolungama ndiye maziko mpaka kalekale.*+
19 Taonani! Mphepo yamkuntho yochokera kwa Yehova idzawomba. Mkwiyo wake udzawomba ngati kamvulumvulu wamphamvu.+ Udzawomba pamitu ya anthu oipawo.+