Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+ Salimo 58:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Miphika yanu isanayambe kumva kutentha kwa moto wa mitengo yaminga,+Mulungu adzauluza ndi mphepo yamkuntho mitengo yaiwisi yaminga pamodzi ndi imene ikuyaka.+ Yesaya 40:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwo sanabzalidwe n’komwe ndipo sanafesedwe. Chitsa chawo sichinazike mizu munthaka.+ Munthu akhoza kungowauzira iwo n’kuuma,+ ndipo mphepo yamkuntho idzawauluza ngati mapesi.+
10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+
9 Miphika yanu isanayambe kumva kutentha kwa moto wa mitengo yaminga,+Mulungu adzauluza ndi mphepo yamkuntho mitengo yaiwisi yaminga pamodzi ndi imene ikuyaka.+
24 Iwo sanabzalidwe n’komwe ndipo sanafesedwe. Chitsa chawo sichinazike mizu munthaka.+ Munthu akhoza kungowauzira iwo n’kuuma,+ ndipo mphepo yamkuntho idzawauluza ngati mapesi.+