Salimo 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Sapereka ndalama zake kuti alandire chiwongoladzanja,+Ndipo salandira chiphuphu kuti akhotetse mlandu wa munthu wosalakwa.+Wochita zinthu zimenezi, sadzagwedezeka konse.+ Mateyu 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+ 1 Timoteyo 6:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndiponso asunge+ maziko abwino+ a tsogolo lawo monga chuma, kuti agwire mwamphamvu moyo weniweniwo.+
5 Sapereka ndalama zake kuti alandire chiwongoladzanja,+Ndipo salandira chiphuphu kuti akhotetse mlandu wa munthu wosalakwa.+Wochita zinthu zimenezi, sadzagwedezeka konse.+
24 “Chotero aliyense wakumva mawu angawa ndi kuwachita adzafanizidwa ndi munthu wochenjera, amene anamanga nyumba yake pathanthwe.+
19 ndiponso asunge+ maziko abwino+ a tsogolo lawo monga chuma, kuti agwire mwamphamvu moyo weniweniwo.+