Salimo 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+ Salimo 112:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi munthu wotero sadzagwedezeka ngakhale pang’ono.+ ל [Laʹmedh]Wolungama adzakumbukiridwa mpaka kalekale.+ Miyambo 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Wolungama sadzagwedezedwa mpaka kalekale,+ koma anthu oipa sadzapitiriza kukhala padziko lapansi.+
8 Ndaika Yehova patsogolo panga nthawi zonse.+Popeza kuti ali kudzanja langa lamanja, sindidzagwedezeka.+
6 Ndithudi munthu wotero sadzagwedezeka ngakhale pang’ono.+ ל [Laʹmedh]Wolungama adzakumbukiridwa mpaka kalekale.+
30 Wolungama sadzagwedezedwa mpaka kalekale,+ koma anthu oipa sadzapitiriza kukhala padziko lapansi.+