Salimo 37:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ochita zoipa adzaphedwa.+Koma oyembekezera Yehova ndi amene adzalandire dziko lapansi.+ Mateyu 21:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+
41 Iwo anayankha kuti: “Chifukwa chakuti ndi oipa, adzawawononga koopsa+ ndipo munda wa mpesawo adzaupereka kwa alimi ena, amene angam’patse zipatso m’nyengo yake.”+