Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+ Ekisodo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+ Deuteronomo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Lero ndichititsa anthu a mitundu ina okhala pansi pa thambo, amene adzamva za inu, kuchita nanu mantha kwambiri ndi kuyamba kukuopani. Chifukwa cha inu, iwo adzanthunthumira ndi kumva zopweteka zofanana ndi zowawa za pobereka.’+
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
27 “Iwe usanafike, ndidzachititsa anthu kumva za ine+ ndipo adzanjenjemera. Ndidzasokoneza anthu onse amene udzawapeze. Adani ako onse adzachita mantha ndipo adzathawa.*+
25 Lero ndichititsa anthu a mitundu ina okhala pansi pa thambo, amene adzamva za inu, kuchita nanu mantha kwambiri ndi kuyamba kukuopani. Chifukwa cha inu, iwo adzanthunthumira ndi kumva zopweteka zofanana ndi zowawa za pobereka.’+