Miyambo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usamasirire anthu oipa,+ ndipo usamasonyeze kuti ukusirira kukhala pagulu lawo,+ Yesaya 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu. Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+
11 Inu Yehova, dzanja lanu lakwezeka,+ koma iwo sakuliona.+ Iwo adzaona mmene mukudziperekera kwa anthu anu, ndipo adzachita manyazi.+ Ndithu, moto+ wanu udzanyeketsa adani anu.
9 Ndani ali ndi nzeru kuti amvetse zinthu zimenezi?+ Wochenjera ndani kuti adziwe zimenezi?+ Pakuti njira za Yehova ndi zowongoka+ ndipo anthu olungama ndi amene adzayendamo,+ koma olakwa adzapunthwa m’njira zimenezo.+