2 Mbiri 20:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mantha+ ochokera kwa Mulungu anagwira mafumu onse a m’dzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli.+ Zekariya 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu nonsenu, khalani chete pamaso pa Yehova,+ pakuti iye wanyamuka+ m’malo ake oyera okhalamo.+
29 Mantha+ ochokera kwa Mulungu anagwira mafumu onse a m’dzikolo atamva kuti Yehova wagonjetsa adani a Isiraeli.+