Salimo 79:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+ Salimo 85:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+ Aroma 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+
5 Haa! Inu Yehova, mukhala wokwiya mpaka liti? Kwamuyaya?+Kodi mkwiyo wanu udzakhala ukuyaka ngati moto mpaka liti?+
85 Inu Yehova, mwasangalala ndi dziko lanu.+Mwabwezeretsa ana a Yakobo amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina.+
11 Ndiye ndifunse kuti, kodi Mulungu anakana anthu ake?+ Ayi ndithu! Paja inenso ndine Mwisiraeli,+ wa mbewu ya Abulahamu, wa fuko la Benjamini.+