Deuteronomo 32:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Izi zili choncho chifukwa anthu inu munachita mosakhulupirika kwa ine+ pakati pa ana a Isiraeli, kumadzi a pa Meriba+ ku Kadesi, m’chipululu cha Zini. Ndiponso chifukwa chakuti anthu inu simunandilemekeze pakati pa ana a Isiraeli.+ Salimo 105:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Anatsegula thanthwe ndipo panatuluka madzi ambiri.+Madziwo anayenda ngati mtsinje kudutsa m’dera lopanda madzi.+ 1 Akorinto 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ndipo onse anamwa chakumwa chimodzimodzi chauzimu.+ Pakuti anali kumwa pathanthwe lauzimu+ limene linali kuwatsatira, ndipo thanthwelo+ linatanthauza Khristu.+ Aheberi 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Tichite zimenezi pamene Malemba akunena kuti: “Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+ musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima.”+
51 Izi zili choncho chifukwa anthu inu munachita mosakhulupirika kwa ine+ pakati pa ana a Isiraeli, kumadzi a pa Meriba+ ku Kadesi, m’chipululu cha Zini. Ndiponso chifukwa chakuti anthu inu simunandilemekeze pakati pa ana a Isiraeli.+
41 Anatsegula thanthwe ndipo panatuluka madzi ambiri.+Madziwo anayenda ngati mtsinje kudutsa m’dera lopanda madzi.+
4 ndipo onse anamwa chakumwa chimodzimodzi chauzimu.+ Pakuti anali kumwa pathanthwe lauzimu+ limene linali kuwatsatira, ndipo thanthwelo+ linatanthauza Khristu.+
15 Tichite zimenezi pamene Malemba akunena kuti: “Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+ musaumitse mitima yanu ngati mmene zinakhalira pamene makolo anu anandipsetsa mtima.”+