Salimo 47:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Ombani m’manja anthu nonsenu.+Fuulirani Mulungu mokondwera chifukwa chakuti wapambana.+ Salimo 95:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+ Salimo 98:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+
95 Bwerani tifuule kwa Yehova mokondwera!+Iye amene ndi Thanthwe la chipulumutso chathu, timufuulire mosangalala chifukwa wapambana.+
4 Fuulirani Yehova mosangalala chifukwa wapambana, inu nonse anthu a padziko lapansi.+Kondwerani, fuulani mosangalala ndi kuimba nyimbo zomutamanda.+