Salimo 78:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Iye anali kukumbukira nthawi zonse kuti iwo ndi anthu athupi la nyama,+Anali kukumbukira kuti moyo wawo umachoka ndipo subwereranso.+ Salimo 89:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Kumbukirani utali wa moyo wanga.+Kodi ana onse a anthu munawalenga pachabe?+
39 Iye anali kukumbukira nthawi zonse kuti iwo ndi anthu athupi la nyama,+Anali kukumbukira kuti moyo wawo umachoka ndipo subwereranso.+