Numeri 33:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ananyamuka ku Ramese+ m’mwezi woyamba,+ pa tsiku la 15. Pasika anali atachitika dzulo lake,+ pamene ana a Isiraeli ananyamuka molimba mtima* pamaso pa Aiguputo onse.+ Machitidwe 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Anakweza anthu amenewa pamene anali kukhala m’dziko lachilendo la Iguputo, ndipo anawatulutsa mmenemo ndi dzanja lokwezeka.+
3 Ananyamuka ku Ramese+ m’mwezi woyamba,+ pa tsiku la 15. Pasika anali atachitika dzulo lake,+ pamene ana a Isiraeli ananyamuka molimba mtima* pamaso pa Aiguputo onse.+
17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Anakweza anthu amenewa pamene anali kukhala m’dziko lachilendo la Iguputo, ndipo anawatulutsa mmenemo ndi dzanja lokwezeka.+