Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 43:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndidzauza kumpoto kuti,+ ‘Abwezere kwawo!’ ndipo ndidzauza kum’mwera kuti, ‘Usawakanize! Bweretsa ana anga aamuna kuchokera kutali, ndi ana anga aakazi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+

  • Yeremiya 31:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ine ndikuwabweretsa kuchokera kudziko la kumpoto,+ ndipo ndikuwasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumalekezero a dziko lapansi.+ Pakati pawo padzakhala anthu akhungu, olumala, akazi apakati komanso akazi amene atsala pang’ono kubereka.+ Adzabwerera kumalo ano ali mpingo waukulu.+

  • Ezekieli 39:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Ndikadzawabweretsa kuchokera ku mitundu ina ya anthu ndi kuwasonkhanitsa pamodzi kuchokera kumayiko a adani awo,+ ndidzadziyeretsa pakati pawo pamaso pa mitundu yambiri ya anthu.’+

  • Luka 13:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Komanso, anthu adzabwera kuchokera kumbali za kum’mawa ndi kumadzulo, kumpoto ndi kum’mwera,+ ndipo adzadya patebulo mu ufumu wa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena