Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 6:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Aisiraeli akalima minda yawo,+ Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kum’mawa+ anali kubwera kudzawaukira.

  • 2 Mafumu 10:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.

  • 2 Mafumu 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yehoahazi sanatsale ndi anthu alionse kupatulapo amuna 50 okwera pamahatchi, magaleta 10, ndi asilikali 10,000 oyenda pansi,+ chifukwa mfumu ya Siriya inawawononga+ ndi kuwapondaponda ngati fumbi la popunthira mbewu.+

  • 2 Mbiri 15:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 M’masiku amenewo, anthu sankayenda mwamtendere+ chifukwa panali zisokonezo zambiri pakati pa anthu onse okhala m’madera a m’dzikoli.+

  • Yeremiya 51:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Nebukadirezara mfumu ya Babulo wandidya.+ Wandisokoneza ndi kundisandutsa chiwiya chopanda kanthu. Wandimeza ngati chinjoka chachikulu.+ Wakhuta zinthu zanga zokoma ndipo wanditsukuluza.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena