Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 27:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ngati ndikanakhala wopanda chikhulupiriro poona ubwino wa Yehova m’dziko la anthu amoyo, ndikanataya chiyembekezo.+

  • Salimo 142:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Ndinafuula kwa inu kuti mundithandize, inu Yehova.+

      Ndinanena kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga,+

      Gawo langa+ m’dziko la amoyo.”+

  • Mlaliki 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti amoyo amadziwa kuti adzafa,+ koma akufa sadziwa chilichonse.+ Iwo salandiranso malipiro alionse, chifukwa zonse zimene anthu akanawakumbukira nazo zaiwalika.+

  • Yesaya 38:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndanena kuti: “Sindidzamuona Ya.* Ndithu Ya sindidzam’penya m’dziko la amoyo.+

      Anthu sindidzawaonanso. Ndidzakhala ndi anthu okhala kudziko limene kulibe moyo.

  • Yesaya 53:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iye anaponderezedwa ndipo anatengedwa popanda kuweruzidwa mwachilungamo.+ Ndani amene anaganizira tsatanetsatane wa mibadwo ya makolo ake?+ Pakuti iye anadulidwa+ m’dziko la amoyo.+ Chifukwa cha zolakwa+ za anthu anga, iye anakwapulidwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena