Zekariya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+ Luka 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kuti zimene anthu ambiri akuganiza mumtima mwawo zionekere poyera.+ Koma iwe lupanga lalitali lidzalasa moyo wako.”+ Aroma 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Popeza pamene tinali ofooka,+ Khristu anafera anthu osapembedza Mulungu pa nthawi yoikidwiratu.+ Aheberi 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Zikanatero, akanavutika mobwerezabwereza kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa.+ Koma tsopano iye waonekera+ kamodzi+ kokha pa mapeto a nthawi* zino+ kuti achotse uchimo kudzera mu nsembe yake.+
7 “Iwe lupanga, nyamuka ukanthe m’busa wanga.+ Ukanthe mwamuna wamphamvu yemwe ndi mnzanga,”+ watero Yehova wa makamu. “Ipha m’busa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+ Ine ndidzakomera mtima nkhosa zonyozeka.”+
35 kuti zimene anthu ambiri akuganiza mumtima mwawo zionekere poyera.+ Koma iwe lupanga lalitali lidzalasa moyo wako.”+
26 Zikanatero, akanavutika mobwerezabwereza kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa.+ Koma tsopano iye waonekera+ kamodzi+ kokha pa mapeto a nthawi* zino+ kuti achotse uchimo kudzera mu nsembe yake.+