Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ngati kutumikira Yehova kukukuipirani, sankhani lero amene mukufuna kum’tumikira,+ kaya milungu imene makolo anu amene anali kutsidya lina la Mtsinje anatumikira,+ kapena milungu ya Aamori amene mukukhala m’dziko lawo.+ Koma ine ndi a m’nyumba yanga, tizitumikira Yehova.”+

  • Miyambo 12:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Milomo yonama imam’nyansa Yehova,+ koma anthu ochita zinthu mokhulupirika amam’sangalatsa.+

  • Miyambo 28:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+

  • 1 Akorinto 4:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Komanso pamenepa, chofunika kwa woyang’anira+ ndicho kukhala wokhulupirika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena