Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ 2 Petulo 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo monga yoyamba ija,+ ndikulimbikitsa mphamvu zanu zotha kuganiza bwino mwa kukukumbutsani,+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
3 Okondedwa, iyi tsopano ndi kalata yachiwiri imene ndikukulemberani, ndipo monga yoyamba ija,+ ndikulimbikitsa mphamvu zanu zotha kuganiza bwino mwa kukukumbutsani,+