1 Samueli 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+ Danieli 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pa nthawi imeneyo Danieli analankhula mwanzeru ndi mozindikira+ kwa Arioki mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali atanyamuka kale kuti akaphe amuna anzeru a m’Babulo.
33 Iwenso udalitsike chifukwa cha kulingalira bwino kwako.+ Udalitsike chifukwa cha kundigwira lero kuti ndisapalamule mlandu wamagazi+ ndi kudzipulumutsa ndekha ndi dzanja langa.+
14 Pa nthawi imeneyo Danieli analankhula mwanzeru ndi mozindikira+ kwa Arioki mkulu wa asilikali olondera mfumu, amene anali atanyamuka kale kuti akaphe amuna anzeru a m’Babulo.