Yobu 13:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma amuna inu ndinu onamizira anzanu.+Nonsenu ndinu madokotala opanda phindu.+ Salimo 86:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Mulungu, anthu odzitukumula andiukira.+Khamu la anthu opondereza anzawo likufunafuna moyo wanga,+Ndipo sanakuikeni patsogolo pawo.+ Salimo 109:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+ Salimo 119:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anthu odzikuza andinyoza koopsa.+Koma ine sindinapatuke pa chilamulo chanu.+
14 Inu Mulungu, anthu odzitukumula andiukira.+Khamu la anthu opondereza anzawo likufunafuna moyo wanga,+Ndipo sanakuikeni patsogolo pawo.+
2 Munthu woipa ndiponso munthu wachinyengo andinenera zoipa ndi pakamwa pawo.+Iwo anena za ine ndi lilime lonama.+ Salimo 119:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anthu odzikuza andinyoza koopsa.+Koma ine sindinapatuke pa chilamulo chanu.+